1 Kings 14:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pita, kamuuze Yerobowamu kuti Chauta, Mulungu wa Israele, akuti, ‘Ine ndidakukweza pakati pa anthu, ndipo ndidakusandutsa mtsogoleri wa anthu anga a ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kauze Yerobowamu, Atero Yehova Mulungu wa Israele, Ndingakhale ndinakukulitsa pakati pa anthu, ndi kukukhalitsa pakati pa anthu ndi kukukhalitsa mfumu ya anthu anga Aisraele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pita, kamuwuze Yeroboamu kuti Yehova Mulungu wa Israeli akuti, ‘Ine ndinakukweza pakati pa anthu ndipo ndinakuyika kukhala mtsogoleri wa anthu anga Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kauze Yerobiamu, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ndingakhale ndinakukulitsa pakati pa anthu, ndi kukukhalitsa mfumu ya anthu anga Aisrayeli,