1 Kings 15:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka cha 18 cha ufumu wa Yerobowamu mwana wa Nebati, Abiya adaloŵa ufumu wa ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha mfumu Yerobowamu mwana wa Nebati, Abiya analowa ufumu wa Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Yeroboamu mwana wa Nebati, Abiya anakhala mfumu ya Yuda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca mfumu Yerobiamu mwana wa Nebati, Abiya analowa ufumu wa Yuda.