1 Kings 15:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akachisi okha opembedzerapo mafano sadaŵaononge. Komabe mtima wa Asa udakhala wokhulupirika kwa Chauta masiku onse a moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma misanje sanaichotse, koma mtima wa Asa unali wangwiro ndi Yehova masiku ake onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale sanachotse malo opembedzerapo mafano, mtima wa Asa unali wodzipereka kwathunthu kwa Yehova masiku onse a moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma misanje sanaicotsa, koma mtima wa Asa unali wangwiro ndi Yehova masiku ace onse.