1 Kings 15:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panali nkhondo pakati pa Asa ndi Baasa, mfumu ya ku Israele, nthaŵi yonse ya ufumu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali nkhondo pakati pa Asa ndi Baasa mfumu ya Israele masiku ao onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panali nkhondo pakati pa Asa ndi Baasa mfumu ya Israeli nthawi yonse ya ulamuliro wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali nkhondo pakati pa Asa ndi Basa mfumu ya Israyeli masiku ao onse.