1 Kings 15:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakhala mfumu mu Yerusalemu zaka zitatu. Mai wake anali Maaka, mwana wa Abisalomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakhala mfumu zaka zitatu m'Yerusalemu, ndipo dzina la amake linali Maaka mwana wa Abisalomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka zitatu. Amayi ake anali Maaka, mwana wa Abisalomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakhala mfumu zaka zitatu m'Yerusalemu, ndipo dzina la amace linali Maaka mwana wa Abisalomu.