1 Kings 15:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide kholo lake. Mwana wake Yehosafati ndiye adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Asa ndi makolo ake, naikidwa kwa makolo ake m'mudzi wa Davide kholo lake; ndipo Yehosafati mwana wake analowa ufumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Asa anamwalira nayikidwa mʼmanda momwe anayikidwa makolo ake mu mzinda wa Davide kholo lake. Ndipo Yehosafati mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Asa ndi makolo ace, naikidwa kwa makolo ace m'mudzi wa Davide kholo lace; ndipo Yosafati mwana wace analowa ufumu m'malo mwace.