1 Kings 15:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baasa adapha Nadabu pa chaka chachitatu cha ufumu wa Asa wa ku Yuda, naloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde Baasa anamupha chaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, nalowa ufumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baasa anapha Nadabu mʼchaka chachitatu cha Asa, mfumu ya ku Yuda ndipo analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde Basa anamupha caka cacitatu ca Asa mfumu ya Yuda, nalowa ufumu m'malo mwace.