1 Kings 15:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Abiya adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide. Ndipo Asa mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Abiya ndi makolo ake, namuika anthu m'mudzi wa Davide; Asa mwana wake nalowa ufumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Abiya anamwalira nayikidwa mʼmanda momwe anayikidwa makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndipo Asa, mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Abiya ndi makolo ace, namuika anthu m'mudzi wa Davide; Asa mwana wace nalowa ufumu m'malo mwace.