1 Kings 16:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalankhula kudzera mwa mneneri Yehu, mwana wa Hanani, mau odzudzula Baasa akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova akutsutsa Baasa anadza kwa Yehu mwana wa Hanani, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anayankhula kudzera mwa Yehu mwana wa Hanani, mawu odzudzula Baasa kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova akutsutsa Basa anadza kwa Yehu mwana wa Hanani, nati,