1 Kings 16:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimuri atangoyamba kulamulira, adapha anthu onse a banja la Baasa. Sadamsiyirepo ndi mwamuna mmodzi yemwe mwa apachibale ake kapena abwenzi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atalowa ufumu wake, nakhala pa mpando wachifumu wake, anawakantha onse a m'nyumba ya Baasa, osamsiyira mwana wamwamuna ndi mmodzi yense, kapena wa abale ake, kapena wa mabwenzi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimuri atangoyamba kulamulira, anapha banja lonse la Baasa. Sanasiyepo munthu wamwamuna ndi mmodzi yemwe, wachibale kapena bwenzi lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atalowa ufumu wace, nakhala pa mpando wacifumu wace, anawakantha onse a m'nyumba ya Basa, osamsiyira mwana wamwamuna ndi mmodzi yense, kapena wa abale ace, kapena wa mabwenzi ace.