1 Kings 16:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Zimuri adaononga banja lonse la Baasa monga momwe Chauta adaalankhulira kudzera mwa Yehu mneneri uja. Paja Yehuyo adaadzudzula Baasa
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero Zimiri anaononga nyumba yonse ya Baasa, monga mwa mau a Yehova, amene ananena akumtsutsa Baasa, mwa dzanja la Yehu mneneri,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Zimuri anawononga banja lonse la Baasa, molingana ndi mawu amene Yehova anayankhula motsutsa Baasa kudzera mwa mneneri Yehu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero Zimri anaononga nyumba yonse ya Basa, monga mwa mau a Yehova, amene ananena akumtsutsa Basa, mwa dzanja la Yehu mneneri,