1 Kings 16:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Omuri adachoka ku Gibetoni pamodzi ndi ankhondo ake onse, nakazinga mzinda wa Tiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Omuri anachoka ku Gibetoni, ndi Aisraele onse naye, nakamangira misasa Tiriza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Omuri ndi Aisraeli onse amene anali naye anachoka ku Gibetoni ndi kukazinga Mzinda wa Tiriza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Omri anacoka ku Gibetoni, ndi Aisrayeli onse naye, nakamangira misasa Tiriza.