1 Kings 16:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimuri ataona kuti mzinda walandidwa, adathaŵira ku nsanja yam'kati ya nyumba ya mfumu. Adatentha nyumbayo, iye nafera momwemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunali tsono, pakuona Zimiri kuti nkhondo yalowa m'mudzi, anakwera pa nsanja ya nyumba ya mfumu, nadzitenthera ndi moto nyumba ya mfumu, nafa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimuri ataona kuti mzinda walandidwa, anathawira ku nsanja ya nyumba ya mfumu ndipo anatentha nyumbayo iye ali momwemo. Kotero iyeyo anafa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunali tsono, pakuona Zimri kuti nkhondo yalowa m'mudzi, anakwera pa nsanja ya nyumba ya mfumu, nadzitenthera ndi mota nyumba ya mfumu, nafa;