1 Kings 16:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Israele adagaŵikanso pakati, ena adatsata Tibini mwana wa Ginati, kuti amlonge ufumu, ndipo ena adatsata Omuri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anthu a Israele anagawika pakati, anthu ena anatsata Tibini mwana wa Ginati kumlonga ufumu, ena natsata Omuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Aisraeli anagawikana pakati: theka linatsatira Tibini mwana wa Ginati kuti limulonge ufumu, ndipo theka lina linatsatira Omuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anthu a Israyeli anagawika pakati, anthu ena anatsata Tibini mwana wa Ginati kumlonga ufumu, ena natsata Omri.