1 Kings 16:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 31 cha ufumu wa Asa wa ku Yuda, Omuri adaloŵa ufumu wa dziko la Israele, ndipo adalamulira zaka khumi ndi ziŵiri. Ku Tiriza adalamulirako zaka zisanu ndi chimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka cha makumi atatu ndi chimodzi cha Asa mfumu ya Yuda, Omuri anayamba kukhala mfumu ya Israele, nakhala zaka khumi ndi ziwiri; ku Tiriza anali mfumu zaka zisanu ndi chimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 31 cha Asa mfumu ya Yuda, Omuri anakhala mfumu ya Israeli, ndipo analamulira zaka 12 ndi miyezi isanu ndi umodzi ku Tiriza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka ca makumi atatu ndi cimodzi ca Asa mfumu ya Yuda, Omri anayamba kukhala mfumu ya Israyeli, nakhala zaka khumi ndi ziwiri; ku Tiriza anali mfumu zaka zisanu ndi cimodzi.