1 Kings 16:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito zina zonse za Omuri zimene ankachita, ndi mphamvu zimene adaonetsa, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo machitidwe ena a Omuri anawachita, ndi mphamvu yake anaionetsa, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ntchito zina za Omuri ndi zamphamvu zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Israeli?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo macitidwe ena a Omri anawacita, ndi mphamvu yace anaionetsa, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?