1 Kings 16:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Omuri adamwalira, naikidwa m'manda ku Samariya. Tsono Ahabu mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Omuri ndi makolo ake, naikidwa m'Samariya; ndipo Ahabu mwana wake analowa ufumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Omuri anamwalira nayikidwa mʼmanda amene anayikidwa makolo ake ku Samariya. Ndipo Ahabu mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Omri ndi makolo ace, naikidwa m'Samaria; ndipo Ahabu mwana wace analowa ufumu m'malo mwace.