1 Kings 16:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi ndidzakufafaniza kotheratu pamodzi ndi banja lako lonse, monga m'mene ndidachitira banja la Yerobowamu mwana wa Nebati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
taona, ndidzachotsa psiti Baasa ndi nyumba yake, ndipo ndidzafanizitsa nyumba yako ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, Ine ndatsala pangʼono kuwononga Baasa pamodzi ndi nyumba yake, ndipo ndidzachitira nyumba yake zimene ndinachita pa nyumba ya Yeroboamu mwana wa Nebati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
taona, ndidzacotsa psiti Basa ndi nyumba yace, ndipo ndidzafanizitsa nyumba yako ndi nyumba ya Yerobiamu mwana wa Nebati,