1 Kings 16:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Ahabu adachita zoipa pamaso pa Chauta kupambana mafumu onse akale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ahabu mwana wa Omuri anachimwa pamaso pa Yehova koposa onse adamtsogolerawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahabu mwana wa Omuri anachita zoyipa zambiri pamaso pa Yehova kupambana mafumu onse akale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ahabu mwana wa Omri anacimwa pamaso pa Yehova koposa onse adamtsogolerawo.