1 Kings 16:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga nyumba ku Samariya yopembedzeramo Baala,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nammangira Baala guwa la nsembe m'nyumba ya Baala anaimanga m'Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapangira Baala guwa lansembe mʼnyumba ya Baala imene anamanga ku Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nammangira Baala guwa la nsembe m'nyumba ya Baala anaimanga m'Samaria.