1 Kings 16:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense wa banja la Baasa amene adzafere mu mzinda, agalu adzamudya. Ndipo aliyense amene adzafere ku thengo, mbalame zamumlengalenga zidzamudya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Agalu adzadya aliyense wa Baasa amene adzafera m'mudzi, ndipo amene adzafera m'thengo zidzamudya mbalame za m'mlengalenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Agalu adzadya aliyense wa banja la Baasa amene adzafere mu mzinda, ndipo mbalame za mu mlengalenga zidzadya iwo amene adzafere kuthengo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Agaru adzadya ali yense wa Basa amene adzafera m'mudzi, ndipo amene adzafera m'thengo zidzamudya mbalame za m'mlengalenga.