1 Kings 16:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baasa adamwalira, naikidwa m'manda ku Tiriza. Ndipo Ela mwana wake ndiye adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Baasa ndi makolo ake, naikidwa ku Tiriza; ndipo Ela mwana wake analowa ufumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baasa anamwalira nayikidwa mʼmanda amene anayikidwa makolo ake ku Tiriza. Ndipo Ela mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Basa ndi makolo ace, naikidwa ku Tiriza; ndipo Ela mwana wace analowa ufumu m'malo mwace.