1 Kings 16:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 26 cha ufumu wa Asa wa ku Yuda, Ela mwana wa Baasa adaloŵa ufumu wa ku Israele ku Tiriza, ndipo adalamulira zaka ziŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chaka cha makumi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi cha Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Baasa analowa ufumu wa Israele ku Tiriza, nakhala mfumu zaka ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 26 cha ufumu wa Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Baasa anakhala mfumu ya Israeli, ndipo analamulira ku Tiriza zaka ziwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi cimodzi ca Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Basa analowa ufumu wa Israyeli ku Tiriza, nakhala mfumu zaka ziwiri.