1 Kings 18:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye ine mukuti ndipite ndikamuuze mbuyanga kuti mwabwera?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano mukuti, Kauze mbuye wako kuti Eliya wabwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano mukundiwuza kuti ndipite kwa mbuye wanga ndi kukanena kuti, ‘Eliya wabwera.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano mukuti, Kauze mbuye wako kuti Eliya wabwera.