1 Kings 18:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Eliya adapita kukadziwonetsa kwa Ahabu. Pamenepo nkuti njala itafika pake penipeni ku Samariya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Eliya ananka kukadzionetsa kwa Ahabu. Ndipo njala inali yaikulu m'Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Eliya anapita kukadzionetsa kwa Ahabu. Tsono nthawi imeneyi njala inakula kwambiri mu Samariya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Eliya anamka kukadzionetsa kwa Ahabu. Ndipo njala inali yaikuru m'Samaria.