1 Kings 18:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aneneri a Baalawo ankafuula kwambiri, nadzichekacheka ndi malupanga ndi mipeni potsata miyambo yao, mpaka magazi chuchuchu m'mabalawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakwezadi mau, nadzitema monga makhalidwe ao ndi mipeni ndi nthungo, kuti mwazi wao unali chuchuchu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwo anafuwula kwambiri ndi kudzichekacheka ndi malupanga ndi mikondo, potsata miyambo yawo, mpaka kutuluka magazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakwezadi mau, nadzitema monga makhalidwe ao ndi mipeni ndi nthungo, kuti mwazi wao unali cucucu.