1 Kings 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu Ahabu adaitana Obadiya, amene ankayang'anira zonse za ku nyumba yachifumu. (Ndiye kuti Obadiya ankatumikira Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ahabu anaitana Obadiya woyang'anira nyumba yake. Koma Obadiya anaopa ndithu Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Ahabu anayitana Obadiya amene ankayangʼanira nyumba yake yaufumu. (Obadiya ankaopa Yehova kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ahabu anaitana Obadiya woyang'anira nyumba yace. Koma Obadiya anaopa ndithu Yehova;