1 Kings 18:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Eliya adauza Ahabu kuti, “Pitani mukadye ndi kumwa, pakuti kukumveka mkokomo wa mvula.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Eliya ananena ndi Ahabu, Nyamukani, idyani, imwani; popeza kumveka mkokomo wa mvula yambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Eliya anati kwa Ahabu, “Pitani, kadyeni ndi kumwa, pakuti kukumveka mkokomo wa mvula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Eliya ananena ndi Ahabu, Nyamukani, idyani, imwani; popeza kumveka mkokomo: wa mvula yambiri.