1 Kings 18:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Ahabu ndi Obadiya adagaŵana dzikolo kuti aliyendere. Ahabu adapita mbali ina, Obadiya mbali inanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono iwo awiri anagawana dziko kukaliyendera; Ahabu anadzera njira yake yekha, ndi Obadiya njira ina yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anagawana dziko loti apiteko, Ahabu anapita mbali ina, Obadiya nʼkupita ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono iwo awiri anagawana dziko kukaliyendera; Ahabu anadzera njira yace yekha, ndi Obadiya njira yina yekha.