1 Kings 18:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Obadiya adamufunsa kuti, “Kodi ndachimwa chiyani kuti inu mundipereke ine mtumiki wanu m'manja mwa Ahabu kuti andiphe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye nati, Ndachimwanji kuti mupereka kapolo wanu m'dzanja la Ahabu kundipha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Obadiya anafunsa kuti, “Kodi ndalakwa chiyani kuti inu mupereke mtumiki wanu kwa Ahabu kuti akaphedwe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye nati, Ndacimwanji kuti mupereka kapolo wanu m'dzanja la Ahabu kundipha?