1 Kings 19:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono amene adzapulumuke ku lupanga la Hazaele, Yehu adzamupha. Amene adzapulumuke ku lupanga la Yehu, Elisa adzamupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzachitika Yehu adzamupha amene adzapulumuka ku lupanga la Hazaele; ndi Elisa adzamupha amene adzapulumuka ku lupanga la Yehu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehu adzapha aliyense amene adzapulumuke ku lupanga la Hazaeli, ndipo Elisa adzapha aliyense amene adzapulumuke ku lupanga la Yehu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzacitika Yehu adzamupha amene adzapulumuka ku lupanga la Hazaeli; ndi Elisa adzamupha amene adzapulumuka ku lupanga la Yehu,