1 Kings 19:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Yezebele adatuma munthu kukauza Eliya kuti, “Milungu indilange ngakhale kundipha kumene, ngati sindikupha iweyo maŵa nthaŵi yonga yomwe ino, monga momwe udaphera aneneriwo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono Yezebele anatuma mthenga kwa Eliya, wakuti, Milungu indilange nionjezepo, ngati sindilinganiza moyo wako ndi moyo wa mmodzi wa iwowo mawa nthawi yomwe yino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yezebeli anatuma mthenga kwa Eliya kuti akamuwuze kuti, “Milungu indilange, ndipo indilange koopsa, ngati mawa nthawi ngati yomwe ino sindidzakupha iwe monga unaphera aneneriwo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono Yezebeli anatuma mthenga kwa Eliya, wakuti, Milungu indilange nionjezepo, ngati sindilinganiza moyo wako ndi moyo wa mmodzi wa iwowo mawa nthawi yomwe yino.