1 Kings 19:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Eliya adachita mantha, ndipo adanyamuka nathaŵa kuti apulumutse moyo wake. Adakafika ku Beereseba, mzinda wa ku Yuda, nakasiya mtumiki wake kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye ataona chimenechi, ananyamuka, nathawa kupulumutsa moyo, nafika ku Beereseba wa ku Yuda, nasiya mnyamata wake pamenepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Eliya ataona zimenezi, ananyamuka nathawa kupulumutsa moyo wake. Atafika ku Beeriseba ku Yuda, anasiya mtumiki wake kumeneko,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ataona cimeneci, ananyamuka, nathawa kupulumutsa moyo, nafika ku Beereseba wa ku Yuda, nasiya mnyamata wace pamenepo.