1 Kings 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yoti Davide amwalire itayandikira, adauza mwana wake Solomoni kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuyandikira masiku ake a Davide akuti amwalire, analamulira Solomoni mwana wake, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide ali pafupi kumwalira, analangiza mwana wake Solomoni kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuyandikira masiku ace a Davide akuti amwalire, analamulira Solomo mwana wace, nati,