1 Kings 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adamwalira, naikidwa m'manda mu mzinda wake wa Davideyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa m'mudzi wa Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Davide anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anagona pamodzi ndi makolo ace, naikidwa m'mudzi wa Davide.