1 Kings 2:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adati, “Inuyo mfumu Solomoni sakukanizani, ndiye chonde ndimati mumpemphe kuti andipatse Abisagi, mtsikana wa ku Sunamu uja, kuti akhale mkazi wanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Mundinenere kwa mfumu Solomoni, popeza sakukanizani, kuti andipatse Abisagi wa ku Sunamu akhale mkazi wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adoniya anapitiriza kunena kuti, “Chonde, inu mupemphe mfumu Solomoni kuti andipatse Abisagi wa ku Sunemu kuti akhale mkazi wanga pakuti mukapempha inu sadzakukanizani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Mundinenere kwa mfumu Solomo, popeza sakukanizani, kuti andipatse Abisagi wa ku Sunamu akhale mkazi wanga.