1 Kings 2:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bateseba adati, “Chabwino. Ndikulankhulira kwa mfumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Bateseba anati, Chabwino, ndidzakunenera kwa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Batiseba anayankha kuti, “Chabwino. Ndidzakuyankhulira kwa mfumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Batiseba anati, Cabwino, ndidzakunenera kwa mfumu.