1 Kings 2:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo mfumu Solomoni adalumbira m'dzina la Chauta kuti, “Mulungu andilange koopsa ngati Adoniya saphedwa chifukwa cha zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo mfumu Solomoni analumbira pa Yehova, nati, Mulungu andilange naonjezepo, zedi Adoniya wadziphetsa yekha ndi mau awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Mfumu Solomoni inalumbira mʼdzina la Yehova kuti, “Mulungu andilange ine koopsa ngati Adoniya saphedwa chifukwa cha pempho lakeli!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo mfumu Solomo analumbira pa Yehova, nati, Mulungu andilange naonjezepo, zedi Adoniya wadziphetsa yekha ndi mau awa.