1 Kings 2:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho mfumu Solomoni adatuma Benaya mwana wa Yehoyada, ndipo iye adakamkantha Adoniyayo, naafa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu Solomoni anatuma dzanja la Benaya mwana wa Yehoyada, ndipo anamgwera, namwalira iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mfumu Solomoni inalamula Benaya mwana wa Yehoyada ndipo anakantha Adoniyayo, nafa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu Solomo anatuma dzanja la Benaya mwana wa Yehoyada, ndipo anamgwera, namwalira iye.