1 Kings 2:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Benaya mwana wa Yehoyada adapita nakamkantha Yowabu, nkumupha, ndipo adamuika m'manda ku nyumba yake ku chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo Benaya mwana wa Yehoyada anakwera namkantha iye, namupha; ndipo anaikidwa m'nyumba yakeyake kuchipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Benaya mwana wa Yehoyada anapita kukakantha Yowabu nʼkumupha ndipo anayikidwa mʼmanda mʼnyumba yakeyake ya ku chipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo Benaya mwana wa Yehoyada anakwera namkantha iye, namupha; ndipo anaikidwa m'nyumba yace yace kucipululu.