1 Kings 2:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukadzatuluka ndi kuwoloka mtsinje wa Kidroni, mosapeneka konse udzaphedwa. Magazi ako adzakhala pamutu pako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza tsiku lomwelo lakutuluka iwe ndi kuoloka mtsinje Kidroni, tadziwa ndithu kuti udzafadi, mwazi wako udzakhala pa mutu wa iwe wekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lomwe udzatulukemo ndi kuwoloka Chigwa cha Kidroni, udziwiretu kuti udzafa ndipo magazi ako adzakhala pamutu pako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza tsiku lomwelo lakuturuka iwe ndi kuoloka mtsinje Kidroni, tadziwa ndithu kuti udzafadi, mwazi wako udzakhala pa mutu wa iwe wekha.