1 Kings 2:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adanyamuka pa bulu, napita ku Gati kwa Akisi, kukafunafuna akapolo ake. Simeiyo adapita, ndipo adakaŵatenga akapolo ake aja ku Gati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Simei ananyamuka, namangirira mbereko pa bulu wake, namka ku Gati kwa Akisi kukafuna akapolo ake; namuka Simei, nabwera nao akapolo ake kuchokera ku Gati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi, anakwera bulu wake ndipo anapita kwa Akisi ku Gati kukafunafuna akapolo ake. Choncho Simei anapita ndi kukatenga akapolo ake ku Gati ndipo anabwera nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Simeyi ananyamuka, namangirira mbereko pa buru wace, namka ku Gati kwa Akisi kukafuna aka polo ace; namuka Simeyi, nabwera nao akapolo ace kucokera ku Gati.