1 Kings 2:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta adzandidalitsa ine mfumu Solomoni, ndipo mpando waufumu wa Davide adzaukhazikitsa mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mfumu Solomoni adzadalitsika, ndi mpando wachifumu wa Davide udzakhazikika pamaso pa Yehova ku nthawi yamuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mfumu Solomoni idzadalitsidwa ndipo mpando waufumu wa Davide udzakhazikika pamaso pa Yehova kwamuyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mfumu Solomo adzadalitsika, ndi mpando wacifumu wa Davide udzakhazikika pamaso pa Yehova ku nthawi yamuyaya.