1 Kings 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwe uchite potsata nzeru zako, koma ndithu usalole kuti afe ndi ukalamba ndi kupita ku manda mwamtendere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chita mwa nzeru yako tsono, osalola mutu wake waimvi utsikire kumanda ndi mtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe uchite kwa iye molingana ndi nzeru zako, koma usalole kuti afe ndi ukalamba ndi kupita ku manda mwamtendere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cita mwa nzeru yako tsono, osalola mutu wace waimvi utsikire kumanda ndi mtendere.