1 Kings 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono usamuyese wosalakwa, poti iwe ndiwe munthu wanzeru. Udzadziŵa wekha choyenera kumchita. Ngakhale ndi nkhalamba, aphedwe ndithu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsono, usamuyesera iye wosachimwa, popeza ndiwe munthu wanzeru, ndipo udziwa umo uyenera kumchitira iye, nutsitsire mutu wake waimvi ndi mwazi kumanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano usamuyese ngati munthu wosalakwa. Iwe ndiwe munthu wanzeru. Udzadziwa choti uchite naye. Ngakhale ndi wokalamba, aphedwe ndithu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsono, usamuyesera iye wosacimwa, popeza ndiwe munthu wanzeru, ndipo udziwa umo uyenera kumcitira iye, nutsitsire mutu wace waimvi ndi mwazi kumanda.