1 Kings 20:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Benihadadiyo adauza azondi aja kuti, “Ngati akubwera ndi mtendere, muŵagwire amoyo. Ngatinso akubwera ndi nkhondo, muŵagwirebe amoyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Chinkana atulukira mumtendere, agwireni amoyo; chinkana atulukira m'nkhondo, agwireni, amoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati, “Kaya akubwera mwamtendere kapena mwankhondo, muwagwire amoyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Cinkana aturukira mumtendere, agwireni amoyo; cinkana aturukira m'nkhondo, agwireni amoyo.