1 Kings 20:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Benihadadi adatuma amithenga ake kwa Ahabu mumzindamo kukamuuza mau akuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natumiza mithenga kumudzi kwa Ahabu mfumu ya Israele, nati kwa iye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatuma amithenga ake mu mzindamo kwa Ahabu mfumu ya Israeli, kukanena kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natumiza mithenga lrumudzi kwa Ahabu mfumu ya Israyeli, nati kwa iye,