1 Kings 20:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene chinkafika chaka china chija, Benihadadi adasonkhanitsa gulu lankhondo la Asiriya, napita ku mzinda wa Afeki, kuti akamenyane ndi ankhondo a ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono kunachitika, pakufikanso chaka Benihadadi anamemeza Aaramu nakwera ku Afeki kukaponyana ndi Aisraele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chaka chinacho Beni-Hadadi anasonkhanitsa Aaramu, napita ku Afeki kukamenyana ndi Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono kunacitika, pakufikanso caka Benihadadi anamemeza Aaramu nakwera ku Meld kukaponyana ndi Aisrayeli.