1 Kings 20:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina munthu wina, mmodzi mwa aneneri, atalamulidwa ndi Chauta, adauza mneneri mnzake kuti, “Iwe, menye ndithu, ndakupemba.” Koma mnzakeyo adakana kummenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wina wa ana a aneneri ananena ndi mnzake mwa mau a Yehova, Undikanthe ine. Koma munthuyo anakana kumkantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Molamulidwa ndi Yehova, mmodzi mwa ana a aneneri anawuza mnzake kuti, “Chonde, menye ndi chida chako,” koma mnzakeyo anakana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wina wa ana a aneneri ananena ndi mnzace mwa mau a Yehova, Undikanthe ine, Koma munthuyo anakana kumkantha.