1 Kings 20:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mneneriyo adapeza mneneri mnzake winanso, namuuza kuti, “Chonde, undimenye.” Mnzakeyo adammenyadi, namtematema pomumenyapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amene uja anakomana ndi munthu wina, nati, Undikanthe. Namkantha munthuyu, namtema pomkantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mneneriyo anapeza munthu wina ndipo anamuwuza kuti, “Chonde, menye.” Choncho munthuyo anamumenya ndi kumuvulaza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amene uja anakomana ndi munthu wina, nati, Undikanthe. Namkantha munthuyu, namtema pomkantha.